
A Malawi 31 amangidwa ku Tanzania ndi thambi yowona zolowa ndi zotuluka
Advertisement A Malawi okwana 31 ali m’gulu la anthu omwe amangidwa ndi nthambi yowona zolowa ndi kutuluka kwa anthu ya dziko la Tanzania. Malinga ndi Mkulu wa nthambi ya Immigration mumzinda wa Dar es Salaam, Vincent Haule watsimikizira Malawi24 kuti a …